id
stringclasses
430 values
sentence
stringlengths
9
2.12k
iso639-3
stringclasses
418 values
iso15924
stringclasses
39 values
language
stringclasses
419 values
nya_Latn
Aliyense ali ndi danga lopeza citetezo pa citukuko ca nchito zace za citukuko cosiyana-siyana mokomera dziko.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ali ndi ufulu wofanana pofuna ntchito zoyendetsedwa ndi boma m'dziko lake.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Popeza nkofunikira ngati munthu saumilizidwa kutero, ngati chinthu chamapeto, kugaukira ulamuliro wankhanza ndi kuponderezedwa, kuti ufulu wa munthu utetezedwe ndi malamulo,
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Palibe munthu aliyense amene adzayenera kuzunzidwa mu njira iriyonse pa nthawi ya moyo wace.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Munthu aliyense sayenera kumangidwa, kusungidwa mu ndende kapena kuthamangitsidwa mu dziko lace mosayenera.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Palibe amene adzachitiridwe nkhaza kapena kuzunzidwa kapena kupatsidwa chilango monyozedwa.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Munthu aliyense ali ndi nchito yothandiza kukweza citukuko ca umoyo wa anthu molingana ndi mphamvu yace.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ali oyenera kukhala bata ndi mtendere pa zomuthandiza pa moyo wake m'dziko lake ndi m'maiko mwina momwe ufulu wa chibadwidwe ndi ufulu wina walembedwa m'chikalata chino ungakwaniritsidwe kwathunthu.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Munthu aliyense ali nalo danga kapena ufulu wa cisangalalo ca moyo wace molingana ndi chibvomerezo ca zofuna za lamulo losamalira khalidwe la umoyo wa munthu.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Munthu aliyense adzaphunzitsidwa za kasamalidwe ndi kakulidwe ka umoyo wa munthu ndi kakwezedwe ka ulemu wa munthu ndi ufulu wa umoyo wace. Maphunziro oterewa adzakhala ofuna kukweza umodzi, cikhululukiro ndi ubwenzi pakati pa anthu a maiko, magulu a mipingo ndi ena osiyana-siyana ndiponso kulimbikitsa nchito za bungwe la United Nations pofuna kukhazikitsa mtendere.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Palibe munthu amene adzasungidwe mu ukapolo kapena mwaukapolo; ukapolo ndi malonda a akapolo adzathetsedwa m'njira zonse.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ali ndi ufulu kuchoka m'dziko lililonse kuonjezerapo lake, ndiponso kubwerera ku dziko lake.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Popeza kuti maiko amene ali mamembala a bungweli la United Nations anatsimikiza kugwirizana ndi bungweli pa nchito zokweza ufulu wa munthu pa umoyo wace ndi kutsatira zofunikira zonse mu lamuloli lopereka ufulu weni-weni pa umoyo wa munthu,
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Popeza kumvetsetsa ufulu umenewu nkofunika kwambiri kuti lonjezo limeneli likwaniritsidwe, Choncho, tsopano, Msonkhano, Waukulu,
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ali ndi ufulu kutenga nawo mbali pa zachikhalidwe cha anthu, kusangalala ndi zaluso ndiponso kugawana za sayansi ndi phindu lake.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ali ndi ufulu kuyenda ndi kukhala m'kati mwamalire a dziko lililonse.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Munthu aliyense ayenera kulemekezedwa pa umoyo wace wa mseri (private life), banja kapena nyumba yace ndiponso umoyo wina wa iye yekha, mwinanso kudzudzulidwa pa khalidwe la umoyo wace wa mseri. Aliyense ali nalo danga locinjirizidwa ku khalidwe losokoneza umoyo wace mwa lamulo.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Ndiponso tsankho lina liri lonse monga la malire a maiko, ndale kapena malo opezeka maikowo mosayang' ana pa ulamuliro wace wa dzikolo pai nkhani za ufulu kapena kayendetsedwe ka ulamuliro wace.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Palibe munthu amene adzakhala monga kapolo kapena kugwira nchito yopanda malipiro mokakamizidwa; Ukapolo kapena cibalo sizidzaloledwa ngakhale pang' ono.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ali ndi ufulu wamaganizo, chikumbumtima ndi chipembedzo; ufuluwu ukhudzanso ufulu wotha kusintha chipembedzo kapena chikhulupiliro, ndi mtendere, kaya payekha kapena mogwirizana ndi ena, pagulu kapena mwachinsinsi, kuonetsa chipembedzo kapena chikhulupiliro pophunzitsa, kuchita, kupembedza ndi kutsatira chipembedzocho.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Popeza anthu a mu bungwe la mgwirizano wa maiko (United Nations) m'chikalata chawo (Charter of United Nations) anatsikimikizira chikhulupiliro chawo mu ufulu wa munthu ndi kusasiyanitsa pakati pa mwamuna ndi mkazi ndiponso atsimikiza kupititsa mtsogolo chikhalidwe cha anthu ndi umoyo wao,
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Munthy aliyense ali ndi danga lopereka dandaulo lace lokhudza za ufulu wa moyo wace ku bungwe la padera la cilungamo pofuna kulandira ciweruzo coyenera pa mlandu uli onse umene munthu angapezeke nao.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Mwamuna ndi mkazi wa msinkhu obvomerezeka ali ndi danga lokwatira kapena kukwatiwa ndi kukhala ndi banja kopanda tsankho la mtundu, unzika kapena mpingo. Anthu awiriwa ali ndi danga lomanga banja ndiponso kumasula banja lao.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Munthu aliyense ali ndi ufulu wogwapo pa umoyo wa zisangalalo za magulu a anthu, kusangalala kapena kudzipereka pa nchito zokweza nchito za zisangalalo zosiyana-siyana pakati pa anthu.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Palibe munthu amene ayenera kulandidwa cuma cace mosayenera.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ali ndi ufulu kugwira ntchito, kusankha ntchito yomwe akufuna, kukhala ndi zoyenereza pa ntchito, ndiponso kutetezedwa ku ulova.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ndi ofanana pamaso pa lamulo ndipo ali oyenera kutetezedwa mosasiyanitsa ndi lamulo. Aliyense ali oyenera kutetezedwa ku tsankho la mtundu uliwonse lomwe likututsa chikalata chino kudzanso kuyambitsa tsankho lililonse la mtundu wotere.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Chimodzimodzinso chilango chokhwima kuposa chomwe chidalipo panthawi yolakwira lamuloyo chisaperekedwe.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Munthu aliyense akazengedwa mlandu wofika nao mu khoti, munthuyo ayenera kuyesedwa osacimwa kufikira pataoneka umboni otsimikiza kuti iyeyo anacita cimolo.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Munthu aliyense ogwira nchito ali ndi danga lolandira malipiro okwanira kusamalira banja lace mopatsidwanso thandizo lina la padera losamalira umoyo wace.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ali ndi ufulu kukhala ndi moyo wathanzi payekha kapena ndi banja lake, kuonjezerapo kukhala ndi chakudya, zovala, nyumba ndi chithandizo cha mankhwala ndi zina zofunikla pa umunthu wake, ndiponso ufulu wa chitetezo ngati iye sali pa ntchito, akudwala, walumala, wafedwa, wakalamba, kapena akusowa zofunika pa moyo wake pa zifukwa zimene iye sangathe kuchitapo kanthu.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Zosindikizidwa zonse za chibvomerezo ca lamulo losamalira khalidwe la umoyo wa munthu, sizitanthauza kuti Boma, kagulu ka anthu kapena munthu wina aliyense ali ndi danga kapena ufulu ocita zinthu zina zonse zofuna kuononga cilingo ca chibvomerezoci ai.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Pokwaniritsa ufulu wake wachibadwidwe ndi ufulu wina, aliyense adzakhala ndi malire pokhapokha malamulo atero ndi cholinga chokwaniritsa kuzindikira ndi kulemekeza ufulu wachibadwidwe ndi ufulu wina wa ena ndiponso kukwaniritsa chilungamo, bata ndi kukhala bwino kwa anthu m'dziko lokomera anthu onse.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Munthu aliyense ali nalo danga lodandaula pa khalidwe la umoyo wace ku mabungwe akulu-akulu oyang' ana pa madandaulo osiyana-siyana mu dziko malinga ndi ufulu wa munthu aliyense opatsidwa mwa lamulo pa umoyo wace.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Munthu aliyense ali ndi danga logwapo pa kayendetsedwe ka Boma la dziko lace mwakudzipereka pa nchito zace kapena mwakusankhako atsogoleri olankhulira nchito za Bomalo.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense amene akugwira ntchito ali ndi ufulu kulandira malipiro oyenera otha kumupatsa iye ndi banja lake moyo wodzilemekeza ndiponso, ngati n'kofunika, apeze njira zina zodzitetezera pa umoyo wake.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Munthu aliyense ali ndi ufulu wa kupata maphunziro. Maphunziro oyamba adzayenera kukhala a ulere komanso mokakamiza mwana aliyense kupata maphunzirowa. Maphunziro a nchito za luso adzayenera kupatsidwa kwa aliyense pamene maphunziro a pamwamba adzapatsidwa ku ana molingana ndi nzeru zao.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ali ndi ufulu kupeza mpumulo ndi kusangalala m'maiko ena m'mene angatetezedwe ku nkhaza.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ali ndi ufulu wa chibadwidwe ndi ufulu wina omwe walembedwa m'chikalata chino, mosasiyanitsa m'mjira iliyonse monga mtundu, maonekedwe a khungu, mwamuna kapena mkazi, chiyankhulo, chipembedzo, ndale kapena maganizo ena, dziko lochokera kapena chikhalidwe, katundu ndi chuma, kubadwa kapena m'mene munthu alili.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ali ndi ufulu kutenga nawo mbali pa kayendetsedwe ka dziko lake, mwa iye mwini kapena kudzera mwa nthumwi yosankhidwa mosaumirizidwa.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ali ndi ufulu kuphunzira. Maphunziro akhale aulele makamaka ku pulaimale. Maphunziro a pulaimale akhale oumiliza. Maphunziro a zaluso ndi ena akhale opezeka ndipo maphunziro apamwamba a m'makoleji akhale opezeka kwa aliyense mofanana ndi nzeru zake.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Anthu onse amabadwa aufulu ndiponso ofanana mu ulemu ndi ufulu wao. Iwowa ndi wodalitsidwa ndi mphamvu zoganiza ndi chikumbumtima ndipo achitirane wina ndi mnzake mwaubale.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ali ndi ufulu kukhala ndi moyo, mtendere ndi chitetezo chathupi.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Munthu aliyense ali ndi danga lokhala nzika ya dziko.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ali ndi ufulu kukhala ndi mtundu.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Amuna ndi akazi okhwima m'maganizo ndi mu msinkhu, mosaganizira mtundu, maonkedwe a khungu kapena chipembedzo, ali ndi ufulu kukwatira kapena kukwatiwa ndi kuyamba banja. Iwowa ali ndi ufulu, ofanana pankhani za ukwati, pomwe ali mbanja kudzanso pothetsa banja.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Komatu danga lotereli siridzaperekedwa ku munthu ofuna kulangidwa kaamba ka zolakwa zina zobvomerezedwa ndi bungwe la United Nations.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Munthu aliyense ali ndi danga lokhala membala wa bungwe liri lonse lothandiza pa umoyo wace.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Popeza kusalabadira ndi kunyoza ufulu wa munthu kwachititsa mchitidwe wa nkhaza womwe wakhumudwitsa chikumbumtima cha anthu, ndipo kukhazikitsa kwa dziko m'mene anthu adzasangalale ndi kulankhula za kukhosi ndiponso kukhulupilira mopanda mantha ndi kusowa kwalengezedwa ngati chinthu cha mtengo wapatali chimene anthu wamba amalakalaka.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Munthu aliyense kopanda tsankho liri lonse ali ndi danga lolandira malipiro molingana ndi anzace ogwira nao nchito imodzi.
nya
Latn
Nyanja
nya_Latn
Aliyense ali ndi ufulu kuganiza ndi kulankhula, zakukhosi, ufuluwu ukukhudzanso kukhala ndi maganizo popanda chopinga ndiponso kufufuza, kulandira ndi kufalitsa mauthenga ndi maganizo a mtundu uliwonse kudzera pa wailesi kapena njira ina iliyonse popanda malire.
nya
Latn
Nyanja
kea_Latn
Tudo guenti tem drêto di ser portegido na sê interesse moral e material qui podê stâ ligado na calquer produção di cusas de ciença, di escrita ou di arte di sê lavra.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo pessoa tem drêto di tomâ, parti librimenti, na bida cultural di comunidadi, di gozâ tudo arte e di participâ na porgréss di ciença e na benéfice qui podê resulta di tudo ês cusa li.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Ninguêm podi bem ta ser, arbitràriamenti, privado di sê propriedade.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Ninguêm podê, di calquer manêra, bai sêr lebádo pa prison, ô ficâ na prison, ô ser mandado di castigo pa longe di sê téra. (Es cusa li ê ta tchomado di "exílio").
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Quem qui trabadja tem drêto di tem remuneraçon equitativo e satisfatório pa podê pirmiti pa el e pâ sê família um existença conformi co dignidadi humano e, completado, si for possive, co tudo ôto meio di porteçon social.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Maternidade e infança tem drêto di tem djuda e di ser amparado co muto cudado. Tudo minino qui nacê dénto ô fora di casamento, ta goza di mésmo porteçon social.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Dispôs disso tudo, ninguêm ca podê bem fazê ningum distinçon fundamentado na statuto político, na cusas di tribunal qui ta tchomádo "jurídico", ô internacional, di país ô di naçon undi bu nacê, nim qui esse naçon ô território di naturalidade d’ess péssoa mésmo qui essi país stâ indipendenti, ô stâ dibaxo di ordi di ôto, ô si el stâ libre ô dibaxo di algum limitaçõn di aôtoridadi, qui nu podê tchoma’l "di soberania".
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo arguêm tem drêto di bandônâ calquer téra undi qu’ê stâ, mesmo si ê undi ê nacê, e el tem drêto di bolta para si téra cando el crê.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Nu ta considrâ qui tudo Estado membro dês grupo ta compromête pa pormovê na cooperaçon co Organizaçon di Naçon Unido, quel ruspêto universal e efectivo di drêto e di liberdadi fundamental.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo arguêm tem drêto na liberdadi di reunion e di associaçon co intençon di paz.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Nu ta considrâ qui, disconhecimento e disprezo di drêto di tudo homi e di tudo mudjer lêbanu pa fazê cusas di rundade qui bem raboltâ concença di tudo Humanidadi. Nu sa ta spèrâ pa tchigâ um mundo undi tudo ser humano ta bem podê ser libri di podê papiâ e di crêditâ, liberto di terror e sim medo di pássâ fomi e di miséria. Tudo ês cusa bem ta ser porclamado cuma um inspiraçon muto importanti pâ nôs tudo: pâ homi e pâ mudjer.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo péssoa tem drêto pa tem educaçon. Educaçon débê di ser di graça, pelo menos quel qui ê parcêdo co quel di scóla elementar fundamental. Quel scola elementar ê obrigatóre. E n’es scóla técnica e profissional dêbê di ser pa tudo criança sem distinçon; pa nu èntrâ num scóla superior, el dèbè stâ aberto pâ tudo guenti por igual e, segundo sês capacidadi e sês merecimento.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo ser humano na ês mundo nacê libri e igual na sê dignidade e na sês drêto. Na sês razon e na sês concénça, tudo arguem debê porcêdê pa co tudo guenti na sprito di fraternidadi.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo péssoa tem drêto di fazê parti na direçon di negôce público di sé téra, quer direitamenti ô por intermédi di representanti librementi escodjido.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo arguêm qui ta bem ser pontádo di um acçon di culpa, nu tem qui pensa qu’el stâ nôcenti tó qui si culpa bem ficâ sclarecido dénto di lei na andamento di um porcesso público undi tudo garantia necessário di difésa debê bem ser garantido pâ el.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo guenti, qui ê mom di um sociedádi, tem drêto pâ tem segurança social e el pôdê, dénto di lei, com tudo ligitimidade, exigi satisfaçon di sês drêto economico na sociedádi e di cultura indispensave, graça qui nu tem qui dâ na esforço nacional e na cooperaçon internacional, di harmonia co organizaçon e co recurso di cada país.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Assembleia Geral Nês Assembleia eres ta porclama qui, quel Declaraçon Universal di Dreto di Homi (homi ô mudjer) cuma um ideal comun pa tchiga na tudo pobo e na tudo naçon, pamódi qui, tudo individu e tudo orgão di sociedadi, si ês tenê el constantimenti na sprito, ês debê sforçâ pa, na ensino e na educaçon, ês podi bem disenvolvê ruspêto dês drêto e liberdadi e eres, podi pormovê, co midida porgressive di ordi nacional e internacional, sê reconhecimento e sê aplicaçon universal e efective, tanto na meio di populaçon di própi estado membro cuma naquêl di tudo territóri colocado debaixo di sês jurisdiçon.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Pai co mai tem prioridadi di tem drêto pa scodjê calquer educaçon pâ dâ sês fidjo ô fidja.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo arguêm tem drêto di àndâ pâ tudo lado, e di scôdjê si casa pa morâ dento di um Estado.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Nu ta considrâ qui’ê essencial si nu bem incorája quel disenvolvimemto di relaçon di amizadi di naçon co naçon.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Família ê um elemento natural e fundamental num sociedadi e el tem drêto di ser portegido di sociedadi e di Estado.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo péssoa tem drêto di entrâ na funçon pública di sé téra,ô di sé país.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo nôs é igual diante di lei e, sem distinçon, nu tem drêto pa igual porteçon pa ser difendido dento di lei. Tudo nôs tem drêto di bem ser portegido di mesma manêra, di calquer discriminaçon que podê bem alterâ ès Declaraçon di qui nu sa tâ flâ e contra calquer fomentaçon pa fazê ès discriminaçon.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Um péssoa tem obrigaçon pâ co sê comunidade, fora di onde ê ca tem possibilidadi di tem quel libri e completo desenvolvimento di sê personalidadi.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Ninguêm al pode ser condenado por acçon ô por omisson, si na occasion qu’el ta fazêba el, tudo es cusa ca era proibido dénto di lei di si téra ô di lei internacional. Di mesma manêra um djuiz ca podê sentenciâ castigo más pêsado di quêl que divia di ser na hora qui quel delito baba ta ser fêto.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Casamento ca podê ser cèlèbrado sem libi e pleno consentimento di quês qui sa ta bai ser marido e mudjer na futur.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Em ninhum caso essi drêto e liberdadi ta bem podê ser exercido em contrário di fim e di princípos di Naçon Unido.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Educaçon debê pontâ pa espádjâ um completo expanson di personalidadi di tudo homi co tudo mudjer e pa reforçâ drêto e liberdadi fundamental di tudo homi co tudo mudjer e di liberdadi di más fundamento e ê debê djuda pa nu compreendê midjor quel tolerância e amizadi di naçon co naçon e di tudo grupo racial ou di riligion como tambê quel crescimento di actividadi di Naçon Unido pa conserbâ paz.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo homi di Deus tem drêto di ser conchido na tudo lugar di sê própri péssoa djusto tambê na cusas di tribunal.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo péssoa tem drêto pâ discansa e pa sê lazer e, naturalmente, ê tem limitaçon qui nu ta cêta, qui ê quel di duraçon di trabadjo e di féria, qui ês tem obrigaçon di pagano.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo arguêm tem drêto, sim discriminaçon ninhum, pâ tem salário di harmonia co sê trabadjo. Salário igual pa trabadjo igual.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo péssoa tem drêto di tem liberdadi di pensamento, di concénça e di religion; ês drêto li ta implicâ liberdadi di mudâ di riligion ô di convicçon, asi cumâ quel liberdadi di maniféstâ sê religion ô sê convicçon, si el stâ só, el co el, ô cô ôtos, tanto na meio di público ô em particular, na qu’ê ta fazê sempri, tudo dia, na sê religion e na quêl qui, na Portugal, ês ta tchomâ "ritos".
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Nu ta considrâ qui, riconhecimento di dignidadi qui ta fazê parti di tudo membro di família humano e di sês drêto qui ê igual e qui nu ca podê squecê, nem ficâ separado di el, ê fundamento di liberdadi, di justiça e di paz di riba di ês mundo;
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Ninguêm podê sofrê di intromisson arbitrário na sê bida di el própi, na di sê familia, na domicilio di sel, ô na sê carta di correio, nim el ca podê ser tacádo na si honra e reputaçon. Ninguêm al pôdi tem intromisson arbitrário na si bida di el própi, na si familia, na si casa ô na carta di sel qui bem di correio, e ninguêm podê flâ mal di honra e reputaçon di cada um. Contra tudo ès intromisson ô ataqui, tudo arguêm tem drêto di ser portegido pa lei.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Ninguêm al podê ficâ scrabo ô na catibêro; ficâ scrabo ô tráto di scrabo ê ca pirmitido, di calquer manêra qui bem ta ser.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo ser humano na ês mundo podi invocâ di drêto e di liberdadi qui sa ta ser porclamado nês Declaraçon li, sem distinçon algum di ôto, nomeadamenti, di raça, di cor, si el ê homi ô mudjer, si el tem ôto lingua, di religion ô di ôto crença, di opinion política, ô ôto li, di orija nacional ô social, di fortuna, di undi ê nacê ô di calquer ôto situaçon.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Nu ta considrâ qui um concepçon comum di êssi drêto e liberdadi ê di muto más importança pa podê dâ completo satisfaçon pa essi compromisso.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Ninguêm podi ser obrigado pa fazê parte di calquer associaçon.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo péssoa tem drêto di fundâ co ôtos péssoa, quel sindicato, e di bem filiâ na sindicato qui ta bem difendi sês interessi.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo guenti tem di tem trabadjo, di podê scodjê sê trabadjo, co condiçon igual e qui podê satisfazêl na trabadjo e el podê tem proteçon contra falta di trabadjo. (disemprego)
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo guenti tem drêto pa ricurso efectivo di quêxa na jurisdiçon nacional compitenti, di tudo cusa qu’ê sabê qui tâ violâ nôs drêto qui tem más fundamento e qui é reconhecido na lei ô na Constituiçon.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo péssoa tem drêto pâ bem pô, na plano social e na plano internacional, um órdi qui podê ser capaz di tornâ completamente efectivo tudo drêto e liberdadi qui nu cabà di flâ nês Declaraçon li.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Ninguêm ca podê bem ser torturado nin podê tem castigo, ô bem tem tratamento di brutalidadi, tratamento horrive ou di disonra.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
A partir di idadi nòváti, tudo homi co tudo mudjer tem drêto di cása e di construí sê família sem limitaçon nim di raça, nacionalidadi ô religion. To-qui durâ casamento e na hora di sê separaçon ês dôs tem igual drêto.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo péssoa, individual ô juntamenti, tem drêto di tem sê propriedade.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Ningum disposiçon di êss Declaraçon li, podê bem ta ser intendido di um manêra qui podê bem involvê pa calquer Estado, grupo di guente ô um sô péssoa, quel drêto di bem fazê calquer actividade ô di particâ algum cusa qui podê bem destroncâ drêto e liberdadi qui nu sa tâ cabâ di flâ.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo péssoa qui sa ta ser persiguido tem drêto di porcurâ e di benificiâ di asilo na ôtos naçon.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Tudo individe tem drêto di tem sê nacionalidadi.
kea
Latn
Kabuverdianu
kea_Latn
Vontadi di pôbo ê quel licérce di ôtoridadi di poder di público; ê debe mostráno-el co eleiçon sério qui ta bem ser fêto, na tempo marcado, por votaçon geral na condiçon di igualdadi co voto sicreto ô si-ma-dja um processo equivalenti podi garanti liberdadi di voto.
kea
Latn
Kabuverdianu